anandipatsa chikondi chosowa
mwana mkazi ine chim'tima kuda bii
monga wakhungu kulephera kupenya
ine uchitsilu chim'chenga m'maso waa
ndinapusa ndi mtima wanga
ouma monga mwala ine kupwalala
pozindikira linali tsiku
ankanka kwao kumangoni ine nkhawa bii
juila julia usatelo
julia julia bwerera
ndikagona ndimangolota kuti mwina iye adzabweranso
nthawi zambiri ndikakhala
ndimalira kunong'oneza bondo
ndikanadziwa nkanamupatsa chikondi changa chonse
ndi mtima wanga wonse
nkanamupatsa moyo wanga
bwezi ndithu mpaka lero tikadali limodzi
juila julia juila julia usatelo
juila julia julia julia bwerera
ambirife tikapeza chikondi timatayilira
timayiwalanso
kuti n'cham'tengo wapatali
ukapeza chikondi n'chofunika kuchisamalira
poti monga dzira
sichichedwa kusweka
Warm Heart of Africa еще тексты
Оценка текста
Статистика страницы на pesni.guru ▼
Просмотров сегодня: 3